Anthu a m’mudzi wina mdera la Mfumu Mabulabo mboma la Mzimba anafa ndi phwete pamene mkulu wina anamenyedwa ndi mwana wachichepere chifukwa chozemba kubweza...
Mkulu wina kwa Wimbe mboma la Kasungu wazunguzia mutu munthu wina yemwe sakudziwika atagwira njoka yake yokawa.
Nkhaniyi ikuti mkuluyo ndi nkhalakale pa bizinesi koma...
Mtsikana wina yemwe amagwila ntchito ya uphunzitsi pa sukulu ina ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota akulila usiku ndi usana mai ake omubala atamuthetsela banja.
Nkhani-yi...